Listen to Ukununkhila (feat. Achina Gattah Ase & Hayze Engola) by Crispy Malawi

Ukununkhila (feat. Achina Gattah Ase & Hayze Engola)

Crispy Malawi

Hip-Hop/Rap

186 Shazams

Lyrics

How many Times Should I tell You? Kuti ndimakufila Ndikungofuna Tizi Tchira Ukudripa ndikumila Fe fe fe fe UKununkhila Ma Guy mwandilira Ngati Mmaona Chithako chi muzachigwira Pa corner ndakupanilira Mmh ndakumatilira Sindiku tripa kuyankha Text phone yangothima Bend Down Ngati Ukulima Kuthoka za Chilima Ine ndikulima Mmmh mmh don't holla Please! Ndili High ndadya Cannabis Ati Spe What is This? Ukugwira Ass koma ufuna Kiss? Hit n Run i never Miss Ndikablowa imakhala Kiss Eeeh ndimakhala Busy Nde USAndipase Busy Ndikuuze Kangati? Kuti ndimakuFila Ndikungofuna TiziTchila Uku Dripa ndiku Mila Fe fe fe fe UKunukhila Fe Fe Fe Fe Ukununkhila Ndikuuze Kangati? Kuti ndimakuFila Ndikungofuna TiziTchila Uku Dripa ndiku Mila Fe fe fe fe UKunukhila Fe Fe Fe Fe Ukununkhila Uli fly sukufunika Visa Life is Too Short ngati Teaser Ndili busy Minding my Business Makape Ali mmadzi tikuwabatiza We in The Cut ngati ndi Scissors Wavala Bum short ndima Lipha Ndango Rocker Zima Yeezus Tili Mangochi walking on Water Ndikungozifila Ngati Jesus Splash! Shes better Than my Ex Chi Body Cha Bho Tipange invest Ndikuuze Kangati? Kuti ndimakufila Ndikungofuna TiziTchila Uku Dripa ndiku Mila Fefefefe UKunukhila FefeFefe Ukununkhila Ndikuuze Kangati? Kuti ndimakuFila Ndikungofuna TiziTchila Uku Dripa ndiku Mila Fe fe fe fe UKunukhila FeFeFeFe Ukununkhila Yo Ndikuuze kangati? Kutindimakufila Sindinakuuze dzina Chifukwa umandidziwa Kaya uli ndi mamuna ndikungofuna kugwira Zoti sukufuna sindikufuna Kudziwa Tivaye pa Awiri bwanji? Panotu pali phokoso Kuvaya pafupi kangonunkhila ka Mafioso(Fe Fe!) Kuvaya ku date moti kazidya Busy ma photo Zonse ndi chabe man bola kugwidwa ndi dolo Ndikuuze kangati? Kodi iwe Jahmeera? Tikukufuna ndi angati? Ndikungofuna Kudziwa Undimvetse ndikamati Hayze akungotchira Unakandifunsa ine ndikanati Ndakumangilira Ndikumasula Asavutike kumayankhula Ndikuziwa ali ndi Freed Mfana Ophusha Mnamuziwa kale kale Akumwa Shooter USAkhale Ngati sukufuna Mfana Ophula Ndikuuze Kangati? Kuti ndimakuFila Ndikungofuna TiziTchila Uku Dripa ndiku Mila Fe fe fe fe UKunukhila Fe Fe Fe Fe Ukununkhila Ndikuuze Kangati? Kuti ndimakuFila Ndikungofuna TiziTchila Uku Dripa ndiku Mila Fe fe fe fe UKunukhila Fe fe fe fe. Ukununkhila
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out