Lyrics

O-B-K beats baby Mmh ma ma ah Ma ma ah Ma ma ma Mmh ah yeah eh eh eh Ngati Black Nina Mkono wakowo tingowudula Kuti usamandikhudzenso, usamandikhudzenso Ngati Sonyezo Mbina yakoyo tingoyepula Kuti usamagwedezenso, usamatsikenso Mmh ngati Lulu, oh ma ma ma ma ma ma Mawu ako usandibwelezelenso, osandibwelezera Ngati Smart, oh ma ma ma ma ma ma Maso ako usandiyang'anenso 'Coz undipweteka Ukaselelera, kusekelera Umamtengo moyo, kumtenga moyo Ukaselelera, kusekelera Umamtengo moyo, kumtenga moyo Uh moyo wanga, (moyo wanga) Moyo wanga nafwa nafwa basi Nafwa basi eh Oh my God akazi ena ine toto Macelba ona ndungolira koto Ndapsa mtima ndatitu ndili pa moto Mkazi wabwino ngatitu ndi wa kumaloto Look how you shine like dynamite Your reflection make i lose my sight eh Unamatamata matamata mtima wanga Oh ma ma ma ma ma ma Mkazi uja wakubelani mwana mwana Zu zu wakuzulura Oh ma ma ma ma ma ma Palibe zokana tibala ana ana Ndati ana Ukaselelera, kusekelera Umamtengo moyo, kumtenga moyo Ukaselelera, kusekelera Umamtengo moyo, kumtenga moyo Uh moyo wanga, (moyo wanga) Moyo wanga nafwa nafwa basi Nafwa basi eh Oh baby, (tembenuka tiyende) Oh darling, (tembenuka tiyende) Oh baby, (tembenuka tiyende) (Tiyende tembenuka tiyende) Oh mamie, (tembenuka tiyende) Oh honey, (tembenuka tiyende) Oh baby, (tembenuka tiyende, tiyende) Ukaselelera, (kusekelera) Kusekelera, (kusekelera) Umamtengo moyo, (umamtengo moyo) Kumtenga moyo, (kumtenga moyo) Ukaselelera, (usekelera) Kusekelera, (usekelera) Umamtengo moyo, (umamtengo moyo) Kumtenga moyo, (ay yeah eh eh) Ukaselelera, (ay yeah eh eh) Kusekelera, (ay yeah eh eh) Umamtengo moyo, (mayi weh eh eh) Kumtenga moyo, (mayi weh eh eh) Ukaselelera, (mayi weh eh eh) Kusekelera, (mayi weh eh eh) Umamtengo moyo, (ah ah ah ah) Kumtenga moyo, (ay ah ah) Oh mamie yeah Oh mamie yeah Umamtenga moyo Kumtenga moyo Oh darling yeah uh liyaliya
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out