Lyrics

Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka ine Mundikumbuke Amayo ndatsala ndeka [repeat 4] Amai asanafe anasiya Mawu Amai asanafe anasiya mawu oooohh Udzafune fune moenda, Bambo ulinawo [repeat 4] Ndili mwana wapancili, wokula NaAmai Ndili mwana wapancili ine, wokula naAmai Ndili wamasiye Wokulila muumpawi Ndili wamasiye wokulila muumpawi Ndili wamasiye ine wokulila muumpawi Ndili wamasiye ine wokulila muumpawi Azimai ancili ana Amasiye mvelani Azimai ancili eh ana amasiye Angazopeni monga ana Anunso Angazopeni monga ana anunso wosataya Angazopeni ye monga ana anunso Angazopeni ye monga ana anunso Chifundo, ndili chifundo Ine Chifundo, ndili chifundo ine Mavhuto, ndili mavhuto ine Mavhuto, ndili mavhuto ine Amai anandilela anamwalila Kale Amai anandilela ine anamwalila kale Poenda ndimangolila, Kukumbuka ondibala Poenda ndimangolila ine, kukumbuka ondibala Pogona Ndimisozi chabe, bambo anga muli kuti inu Pogona ndimisozi chabe, bambo anga muli kuti inu Ndakulila muumpawi, wopatsa chisoni ndithu Ndakulila muumpawi, wopatsa chisoni ndithu Ngati muli Ndiumoyo, kapena munamwalila Ngati muli ndiumoyo, kapena munamwalila Bwanji Osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko Bwanji osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko Chifundo, Ndili chifundo ine Chifundo, ndili chifundo ine Mavhuto, ndili mavhuto ine Mavhuto, ndili mavhuto ine
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out